Yesaya 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa thandizo lochokera ku Iguputo ndi losathandiza ngakhale pangʼono.+ Choncho iye ndamutchula kuti: “Rahabi+ amene amangokhala osachita chilichonse.”
7 Chifukwa thandizo lochokera ku Iguputo ndi losathandiza ngakhale pangʼono.+ Choncho iye ndamutchula kuti: “Rahabi+ amene amangokhala osachita chilichonse.”