-
1 Mbiri 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo nʼkuwakhazika pamalowo. Iwo adzakhala pamenepo ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu oipa sadzawaponderezanso ngati mmene ankachitira kale,+
-