-
Yesaya 9:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ulamuliro* wake udzafika kutali
Ndipo mtendere sudzatha,+
Pampando wachifumu wa Davide+ ndiponso mu ufumu wake
Kuti iye achititse ufumuwo kukhazikika+ ndiponso kukhala wolimba
Pogwiritsa ntchito chilungamo+ ndiponso mtima wowongoka,+
Kuyambira panopa mpaka kalekale.
Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.
-
-
Yeremiya 33:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 “Yehova wanena kuti, ‘Mʼnyumba ya Davide simudzalephera kupezeka munthu woti akhale pampando wachifumu wa nyumba ya Isiraeli.+
-