-
1 Mafumu 11:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Atatero, anauza Yerobowamu kuti:
“Tengapo mapisi 10, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikungʼamba ufumuwu kuuchotsa mʼmanja mwa Solomo ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+
-