-
1 Mafumu 11:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Mwana wake ndidzamʼpatsa fuko limodzi kuti mtumiki wanga Davide apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mumzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha kuti ukhale ndi dzina langa.
-