Salimo 103:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu.+Iye amaphuka ngati duwa lakutchire.+ 1 Petulo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika