Salimo 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mumachititsa kuti nyanja imene ikuchita mafunde ikhale bata.+Mumaletsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+
7 Mumachititsa kuti nyanja imene ikuchita mafunde ikhale bata.+Mumaletsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+