-
Salimo 8:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,
Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+
-
-
Salimo 76:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Inu mumawala kwambiri.*
Ndinu waulemerero kuposa mapiri amene muli nyama zodya zinzake.
-