-
1 Mbiri 16:23-25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Dziko lonse lapansi liimbire Yehova!
Tsiku ndi tsiku muzilengeza za chipulumutso chake!+
24 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,
Lengezani ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.
25 Chifukwa Yehova ndi wamkulu komanso woyenera kutamandidwa,
Iye ndi wochititsa mantha kwambiri kuposa milungu ina yonse.+
-