Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 40:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Salimo 71:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakamwa panga padzanena za chilungamo chanu,+

      Tsiku lonse padzanena za ntchito za chipulumutso chanu,

      Ngakhale kuti nʼzochuluka ndipo sindingathe kuzimvetsa.*+

  • Yesaya 52:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mapazi a munthu amene akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino ndi okongola kwambiri!+

      Munthu amene akulengeza za mtendere,+

      Amene akubweretsa uthenga wabwino wa zinthu zabwino,

      Amene akulengeza za chipulumutso,

      Amene akuuza Ziyoni kuti: “Mulungu wako wakhala Mfumu.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani