Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.* Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala Mfumu!+ Dziko lapansi lisangalale.+ Zilumba zambiri zikondwere.+ Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.*