Salimo 65:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Malo odyetserako ziweto adzaza ndi nkhosa,Ndipo mʼzigwa muli tirigu yekhayekha.+ Malo onsewa akufuula komanso kuimba mosangalala.+
13 Malo odyetserako ziweto adzaza ndi nkhosa,Ndipo mʼzigwa muli tirigu yekhayekha.+ Malo onsewa akufuula komanso kuimba mosangalala.+