1 Mafumu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iweyo ukayenda mʼnjira zanga ngati mmene bambo ako Davide anachitira,+ yemwe anali ndi mtima wokhulupirika+ komanso ankachita zoyenera,+ ukachita zonse zimene ndinakulamula,+ ndiponso ukamamvera malangizo anga ndi ziweruzo zanga,+ Salimo 78:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Anasankha Davide+ mtumiki wake,Ndipo anamuchotsa kumakola a nkhosa,+ Salimo 78:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Iye anawaweta ndi mtima wokhulupirika,+Ndipo anawatsogolera mwaluso.+
4 Iweyo ukayenda mʼnjira zanga ngati mmene bambo ako Davide anachitira,+ yemwe anali ndi mtima wokhulupirika+ komanso ankachita zoyenera,+ ukachita zonse zimene ndinakulamula,+ ndiponso ukamamvera malangizo anga ndi ziweruzo zanga,+
70 Anasankha Davide+ mtumiki wake,Ndipo anamuchotsa kumakola a nkhosa,+ Salimo 78:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Iye anawaweta ndi mtima wokhulupirika,+Ndipo anawatsogolera mwaluso.+