Yobu 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndangotsala mafupa okhaokha,+Ndipo pangʼonongʼono nʼkanafa.* Miyambo 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mtima wosangalala uli ngati mankhwala amene amachiritsa,+Koma munthu akakhumudwa mphamvu zake zimatha.*+
22 Mtima wosangalala uli ngati mankhwala amene amachiritsa,+Koma munthu akakhumudwa mphamvu zake zimatha.*+