Yesaya 60:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Alendo adzamanga mipanda yako,Ndipo mafumu awo adzakutumikira.+Ine ndinakulanga chifukwa ndinali nditakwiya,Koma chifukwa cha kukoma mtima kwanga* ndidzakuchitira chifundo.+
10 Alendo adzamanga mipanda yako,Ndipo mafumu awo adzakutumikira.+Ine ndinakulanga chifukwa ndinali nditakwiya,Koma chifukwa cha kukoma mtima kwanga* ndidzakuchitira chifundo.+