Salimo 147:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova akumanga Yerusalemu.+Akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli amene anapita ku ukapolo.+ Yeremiya 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anatengedwa kupita kudziko lina ndidzawabwezeretsa+ ndipo adzakhalanso ngati mmene analili poyamba.+
7 Anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anatengedwa kupita kudziko lina ndidzawabwezeretsa+ ndipo adzakhalanso ngati mmene analili poyamba.+