Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+ Habakuku 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Chivumbulutso 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+