Salimo 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 48:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Dzanja langa linayala maziko a dziko lapansi,+Ndipo dzanja langa lamanja linatambasula kumwamba.+ Ndikaitana zinthu zimenezi, zimaimirira limodzi. Aheberi 1:10-12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
13 Dzanja langa linayala maziko a dziko lapansi,+Ndipo dzanja langa lamanja linatambasula kumwamba.+ Ndikaitana zinthu zimenezi, zimaimirira limodzi.