-
Yobu 38:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Ndi ndani amene ali wanzeru kwambiri moti angawerenge mitambo,
Kapena ndi ndani amene angapendeketse zosungira madzi zakumwamba?+
-