Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mbiri 16:8-13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Salimo 96:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,

      Lengezani ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+

  • Salimo 145:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo adzalengeza za ulemerero wa ufumu wanu+

      Komanso adzalankhula za mphamvu zanu,+

      ל [Lamed]

      12 Kuti anthu adziwe za ntchito zanu zamphamvu+

      Ndiponso kukula kwa ulemerero wa ufumu wanu.+

  • Yesaya 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Pa tsiku limenelo mudzanena kuti:

      “Yamikani Yehova, itanani pa dzina lake,

      Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake.+

      Lengezani kuti dzina lake ndi lokwezeka.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani