-
Deuteronomo 7:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 musawaope.+ Nthawi zonse muzikumbukira zimene Yehova Mulungu wanu anachitira Farao ndi Iguputo yense.+ 19 Muzikumbukira ziweruzo zamphamvu zimene* maso anu anaona, zizindikiro, zodabwitsa,+ dzanja lamphamvu ndiponso mkono wotambasula umene Yehova Mulungu wanu anagwiritsa ntchito pokutulutsani mʼdzikolo.+ Izi ndi zimene Yehova Mulungu wanu adzachite ndi anthu a mitundu yonse amene mukuwaopa.+
-