-
Nehemiya 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, Mulungu wamkulu komanso wochititsa mantha. Inu mumakwaniritsa pangano lanu ndipo mumasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amakukondani ndi kusunga malamulo anu.+
-