Salimo 78:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anangʼamba miyala mʼchipululu,Anawalola kumwa madziwo mpaka ludzu kutha ngati kuti akumwa madzi amʼnyanja.+ 16 Iye anatulutsa madzi ochuluka pathanthwe,Ndipo anachititsa madzi ambiri kuti ayende ngati mitsinje.+
15 Iye anangʼamba miyala mʼchipululu,Anawalola kumwa madziwo mpaka ludzu kutha ngati kuti akumwa madzi amʼnyanja.+ 16 Iye anatulutsa madzi ochuluka pathanthwe,Ndipo anachititsa madzi ambiri kuti ayende ngati mitsinje.+