-
Salimo 143:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo chifukwa cha dzina lanu.
Ndipulumutseni mʼmavuto anga, chifukwa ndinu wachilungamo.+
-
-
Ezekieli 20:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+
-