Deuteronomo 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munaiwala Thanthwe+ limene linakuberekani,Ndipo simunakumbukire Mulungu amene anakuberekani.+