Yesaya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu mwasiya anthu anu, nyumba ya Yakobo,+Chifukwa iwo ayamba kutsatira miyambo yambiri ya Kumʼmawa.Akuchita zamatsenga+ ngati AfilisitiNdiponso ali ndi ana ambiri a alendo.
6 Inu mwasiya anthu anu, nyumba ya Yakobo,+Chifukwa iwo ayamba kutsatira miyambo yambiri ya Kumʼmawa.Akuchita zamatsenga+ ngati AfilisitiNdiponso ali ndi ana ambiri a alendo.