-
2 Mafumu 21:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Manase anaphanso anthu ambiri osalakwa mpaka magazi awo anadzaza Yerusalemu kuyambira koyambirira mpaka kumapeto,+ kuwonjezera pa tchimo lake lochititsa kuti Ayuda achimwe pochita zoipa pamaso pa Yehova.
-