Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 68:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Anthu amene alibe wowathandiza, Mulungu amawapatsa nyumba kuti azikhalamo.+

      Amamasula akaidi nʼkuwathandiza kuti zinthu ziwayendere bwino.+

      Koma anthu osamvera* adzakhala mʼdziko louma.+

  • Salimo 146:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Amene amaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa anthu amene achitiridwa chinyengo,

      Amene amapereka chakudya kwa anthu anjala.+

      Yehova akumasula anthu amene ali mʼndende.*+

  • Yesaya 49:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova wanena kuti:

      “Pa nthawi yosonyeza kukoma mtima kwanga, ndinakuyankha.+

      Ndipo pa tsiku la chipulumutso ndinakuthandiza.+

      Ndinkakuteteza kuti ndikupereke ngati pangano kwa anthu,+

      Kuti ndikonzenso dzikolo,

      Kuti anthuwo atengenso cholowa chawo chimene chinali bwinja,+

       9 Kuti ndiuze akaidi kuti, ‘Tulukani!’+

      Ndiponso amene ali mumdima+ kuti, ‘Bwerani poyera kuti anthu akuoneni!’

      Iwo adzadya msipu mʼmphepete mwa msewu,

      Ndipo mʼmphepete mwa njira zonse zimene zimadutsidwadutsidwa* mudzakhala malo awo odyeramo msipu.

  • Yesaya 61:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani