-
2 Mafumu 3:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 chifukwa Yehova wanena kuti: “Simuona mphepo kapena mvula, koma mʼchigwa chonsechi mudzaza madzi.+ Ndipo inu pamodzi ndi ziweto zanu komanso nyama zanu zina mumwa madziwo.”’
-
-
Yesaya 35:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Malo ouma chifukwa cha kutentha adzakhala dambo la madzi,
Ndipo malo aludzu adzakhala ndi akasupe amadzi.+
-