-
Salimo 38:19, 20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma adani anga ndi amphamvu kwambiri,
Ndipo odana nane popanda chifukwa anachuluka.
20 Iwo anandibwezera choipa mʼmalo mwa chabwino,
Ndikafuna kuchita zabwino iwo ankandiletsa.
-