Salimo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Adani anga onse amandinyoza,+Makamaka anthu oyandikana nawo. Ndipo anthu ondidziwa amachita nane mantha.Akandiona ndili panja amandithawa.+
11 Adani anga onse amandinyoza,+Makamaka anthu oyandikana nawo. Ndipo anthu ondidziwa amachita nane mantha.Akandiona ndili panja amandithawa.+