-
Salimo 35:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Onsewo achite manyazi nʼkuthedwa nzeru,
Onse amene amasangalala tsoka likandigwera.
Onse amene amadzikweza pamaso panga atsitsidwe ndipo achite manyazi.
-