Salimo 25:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthu amaopa Yehova,+ Iye adzamulangiza njira imene akuyenera kusankha.+ נ [Nun] 13 Moyo wake udzasangalala ndi zinthu zabwino,+Ndipo mbadwa* zake zidzatenga dziko lapansi kuti likhale lawo.+ Salimo 37:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
12 Ngati munthu amaopa Yehova,+ Iye adzamulangiza njira imene akuyenera kusankha.+ נ [Nun] 13 Moyo wake udzasangalala ndi zinthu zabwino,+Ndipo mbadwa* zake zidzatenga dziko lapansi kuti likhale lawo.+