Deuteronomo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mʼdziko lanu mudzapitirizabe kupezeka anthu osauka.+ Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti, ‘Muzikhala owolowa manja kwa mʼbale wanu wovutika komanso wosauka mʼdziko lanu.’+ Miyambo 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
11 Mʼdziko lanu mudzapitirizabe kupezeka anthu osauka.+ Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti, ‘Muzikhala owolowa manja kwa mʼbale wanu wovutika komanso wosauka mʼdziko lanu.’+