Salimo 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inu mumandipatsa chishango chanu chachipulumutso,+Dzanja lanu lamanja limandithandiza,*Ndipo kudzichepetsa kwanu nʼkumene kumandikweza.+ Salimo 138:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 57:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 66:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Dzanja langa ndi limene linapanga zinthu zonsezi,Ndipo izi ndi zimene zinachitika kuti zonsezi zikhalepo,” akutero Yehova.+ “Choncho ine ndidzayangʼana munthu ameneyu,Ndidzayangʼana munthu wodzichepetsa ndiponso wosweka mtima amene amadera nkhawa mawu anga.+
35 Inu mumandipatsa chishango chanu chachipulumutso,+Dzanja lanu lamanja limandithandiza,*Ndipo kudzichepetsa kwanu nʼkumene kumandikweza.+
2 “Dzanja langa ndi limene linapanga zinthu zonsezi,Ndipo izi ndi zimene zinachitika kuti zonsezi zikhalepo,” akutero Yehova.+ “Choncho ine ndidzayangʼana munthu ameneyu,Ndidzayangʼana munthu wodzichepetsa ndiponso wosweka mtima amene amadera nkhawa mawu anga.+