Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Odya bwino ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,

      Koma anjala alibenso njala.+

      Wosabereka wabereka ana 7,+

      Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, ali yekhayekha.*

  • Yesaya 54:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 “Fuula mosangalala iwe mkazi amene sunaberekepo mwana.+

      Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ sangalala ndipo ufuule mosangalala.+

      Chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiri

      Kuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”*+ akutero Yehova.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani