-
Salimo 84:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mphamvu zawo zidzapitiriza kuwonjezeka pamene akuyenda.+
Aliyense wa iwo amaonekera pamaso pa Mulungu mu Ziyoni.
-
-
Salimo 100:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Muyamikeni, tamandani dzina lake.+
-