-
Salimo 97:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Chifukwa inu Yehova, ndinu Wamʼmwambamwamba woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.
Ndinu wokwezeka kwambiri kuposa milungu ina yonse.+
-