-
Salimo 77:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndikuganizira masiku akale,+
Ndikuganizira zaka zakale kwambiri.
-
-
Salimo 111:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
ה [He]
3 Zochita zake zimasonyeza ulemerero ndi ulemu,
ו [Waw]
Ndipo chilungamo chake chidzakhalapobe kwamuyaya.+
-