Salimo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musandibisire nkhope yanu.+ Musabweze mtumiki wanu mutakwiya. Inu ndi amene mumandithandiza.+Musanditaye kapena kundisiya, inu Mulungu amene mumandipulumutsa.
9 Musandibisire nkhope yanu.+ Musabweze mtumiki wanu mutakwiya. Inu ndi amene mumandithandiza.+Musanditaye kapena kundisiya, inu Mulungu amene mumandipulumutsa.