Salimo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndikuitana inu Yehova, Thanthwe langa,+Musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana. Mukakhala chete pamene ndikukuitanani,Ndidzafanana ndi anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
28 Ndikuitana inu Yehova, Thanthwe langa,+Musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana. Mukakhala chete pamene ndikukuitanani,Ndidzafanana ndi anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+