-
Yobu 38:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Ndi ndani amakonzera khwangwala chakudya,+
Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,
Komanso akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?”
-