-
Salimo 25:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
ה [He]
5 Ndithandizeni kuti ndiziyenda mʼchoonadi chanu ndipo mundiphunzitse,+
Chifukwa inu ndinu Mulungu amene mumandipulumutsa.
ו [Waw]
Ndimayembekezera inu tsiku lonse.
-
-
Salimo 27:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende mʼnjira yanu.+
Nditsogolereni mʼnjira yoyenera kuti nditetezeke kwa adani anga.
-