Salimo 62:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana a anthu ali ngati mpweya,Ana a anthu ndi malo othawirako osadalirika.+ Onse pamodzi akaikidwa pasikelo amapepuka kuposa mpweya.+ Salimo 144:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amafanana ndi mpweya.+Masiku a moyo wake ali ngati mthunzi wongodutsa.+
9 Ana a anthu ali ngati mpweya,Ana a anthu ndi malo othawirako osadalirika.+ Onse pamodzi akaikidwa pasikelo amapepuka kuposa mpweya.+