Yobu 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ine ndine wopanda pake.+ Kodi ndingakuyankheni chiyani? Ndaika dzanja langa pakamwa.+ Salimo 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha ndipo sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula ndipo sindikutsegula pakamwa.+
13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha ndipo sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula ndipo sindikutsegula pakamwa.+