2 Samueli 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Ndiye ndi ndani angamufunse kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani ukuchita zimenezi?’”
10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Ndiye ndi ndani angamufunse kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani ukuchita zimenezi?’”