Salimo 90:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mumaika zolakwa zathu patsogolo panu,*+Zinsinsi zathu zaululika chifukwa cha kuwala kwa nkhope yanu.+
8 Mumaika zolakwa zathu patsogolo panu,*+Zinsinsi zathu zaululika chifukwa cha kuwala kwa nkhope yanu.+