Salimo 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inu Yehova, nditetezeni kwa anthu amene akundiimba mlandu.+Menyanani ndi anthu amene akumenyana ndi ine.+ Miyambo 22:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+23 Chifukwa Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+Ndipo adzachotsa moyo wa anthu amene akuwabera mwachinyengo.
35 Inu Yehova, nditetezeni kwa anthu amene akundiimba mlandu.+Menyanani ndi anthu amene akumenyana ndi ine.+
22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+23 Chifukwa Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+Ndipo adzachotsa moyo wa anthu amene akuwabera mwachinyengo.