Salimo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 78:65, 66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Kenako Yehova anadzuka ngati kuti anali mtulo,+Ngati mmene amadzukira munthu wamphamvu+ pambuyo pomwa vinyo wambiri. 66 Iye anathamangitsa adani ake nʼkuwabweza,+Anachititsa kuti adaniwo akhale onyozeka mpaka kalekale.
65 Kenako Yehova anadzuka ngati kuti anali mtulo,+Ngati mmene amadzukira munthu wamphamvu+ pambuyo pomwa vinyo wambiri. 66 Iye anathamangitsa adani ake nʼkuwabweza,+Anachititsa kuti adaniwo akhale onyozeka mpaka kalekale.