Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu+ kuti akupulumutseni ndi kupereka adani anu mʼmanja mwanu. Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu nʼkusiya kuyenda nanu limodzi.

  • Salimo 132:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+

      Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+

  • Yesaya 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Fuulani mwachisangalalo inu okhala mu Ziyoni,*

      Chifukwa Woyera wa Isiraeli amene ali pakati panu ndi wamkulu.”

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani